2 Mafumu 15:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Salumu mwana wa Yabesi analowa ufumu wace caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi zinai ca Uziya mfumu ya Yuda, nakhala mfumu mwezi umodzi m'Samariya.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:5-17