2 Mafumu 14:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nagona Yoasi ndi makolo ace, namuika m'Samariya pamodzi ndi mafumu a Israyeli; nakhala mfumu m'malo mwace Yerobiamu mwana wace.

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:6-25