2 Mafumu 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Amaziya mwana wa Yoasi mfumu ya Yuda anakhala ndi moyo, atamwalira Yoasi mwana wa Yoahazi mfumu ya Israyeli, zaka khumi ndi zisanu.

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:12-19