2 Mafumu 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Macitidwe ena tsono a Yoasi adazicita, ndi mphamvu yace, ndi umo analimbana naye Amaziya mfumu ya Yuda, sizilembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:13-23