1 Samueli 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli analamulira anyamata ace, nati, Mulankhule naye Davide m'tseri, ndi kuti, Taonani mfumu akondwera nanu, ndi anyamata ace onse akukondani; cifukwa cace tsono, khalani mkamwini wa mfumu.

1 Samueli 18

1 Samueli 18:17-24