1 Samueli 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Sauli, Ndidzampatsa iye, kuti amkhalire msampha, ndi kuti dzanja la Afilisti limgwere. Cifukwa cace Sauli ananena ndi Davide, Lero udzakhala mkamwini wanga kaciwiri.

1 Samueli 18

1 Samueli 18:14-23