1 Samueli 1:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthuyo Elikana, ndi a pa banja lace onse, anakwera kukapereka kwa Yehova nsembe ya caka ndi caka, ndi ya cowinda cace.

1 Samueli 1

1 Samueli 1:13-28