1 Samueli 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene nthawi yace inafika, Hana anaima, nabala mwana wamwamuna: namucha dzina lace Samueli, nati, Cifukwa ndinampempha kwa Yehova,

1 Samueli 1

1 Samueli 1:19-26