1 Samueli 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anauka mamawa, nalambira pamaso pa Yehova, nabwerera, nafikanso kwao ku Rama; ndipo Elikana anadziwa mkazi wace Hana, Yehova namkumbukila iye.

1 Samueli 1

1 Samueli 1:10-28