1 Samueli 1:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Hana sadakwera, cifukwa kuti anati kwa mwamuna wace, Sindidzakwerako kufikira mwanayo ataleka kuyamwa, pamenepo ndidzapita naye kuti aoneke pamaso pa Yehova, ndi kukhalako cikhalire.

1 Samueli 1

1 Samueli 1:21-28