1 Mbiri 29:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukulu, ndi mphamvu, ndi ulemerero, ndi kulakika, ndi cifumu ndi zanu, Yehova; pakuti zonse zam'mwamba ndi pa dziko lap ansi ndi zanu; ufumu ndi wanu, Yehova; ndipo mwakwezeka mutu wa pa zonse.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:1-15