1 Mbiri 29:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Davide analemekeza Yehova pamaso pa khamu lonse, nati Davide, Wolemekezedwa Inu, Yehova Mulungu wa Israyeli, Atate wathu ku nthawi zomka muyaya.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:9-11