1 Mbiri 29:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zolemera ndi ulemu zifuma kwanu, ndipo mucita ufumu pa zonse, ndi m'dzanja mwanu muli mphamvu yaikuru; kukuza ndi kupatsa onse mphamvu kuli m'dzanja lanu.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:8-13