1 Mbiri 22:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

taona, udzabala mwana, ndiye adzakhala munthu wa phe; ndipo nelidzampumulitsira adani ace onse pozungulirapo, pakuti dzina lace lidzakhala Solomo; ndipo ndidzapatsa Israyeli mtendere ndi bata masiku ace;

1 Mbiri 22

1 Mbiri 22:3-17