1 Mbiri 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

iyeyu adzamangira dzina langa nyumba; iye adzakhala mwana wanga, ndi Ine ndidzakhala Atate wace; ndipo ndidzakhazikitsa mpando wacifumu wa ufumu wace pa Israyeli kosalekeza.

1 Mbiri 22

1 Mbiri 22:1-19