1 Mbiri 22:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mau a Yehova anandidzera, kuti, Wakhetsa mwazi wocuruka, popeza wacita nkhondo zazikuru; sudzamangira dzina langa nyumba, popeza wakhetsa pansi mwazi wambiri pamaso panga;

1 Mbiri 22

1 Mbiri 22:1-13