1 Mbiri 22:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Solomo mwana wace, Kunena za ine, kumtima kwanga kudati, ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba.

1 Mbiri 22

1 Mbiri 22:1-10