1 Mbiri 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aaramu a ku Damasiko anadza kudzathandiza Hadarezeri mfumu ya Zoba; koma Davide anakantha Aaramu amuna zikwi makumi awiri mphambu ziwiri.

1 Mbiri 18

1 Mbiri 18:1-15