1 Mbiri 18:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide analanda magareta ace cikwi cimodzi, ndi apakavalo zikwi zisanu ndi ziwiri, ndi oyenda pansi zikwi makumi awiri; Davide anadula mitsita akavalo onse okoka magareta, koma anasungako ofikira magareta zana limodzi.

1 Mbiri 18

1 Mbiri 18:3-13