1 Mbiri 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anakantha Hadarezeri mfumu ya Zoba ku Hamati, pomuka iye kukhazikitsa ulamuliro wace ku mtsinje wa Firate.

1 Mbiri 18

1 Mbiri 18:1-4