1 Mbiri 10:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Afilisti tsono analimbana nkhondo ndi Israyeli; ndipo amuna a Israyeli anathawa pamaso pa Afilisti, nagwa ophedwa pa phiri la Giliboa.

2. Ndipo Afilisti anaumirira kutsata Sauli ndi ana ace, ndi Afilistiwo anawapha Yonatani, ndi Abinadabu, ndi Malikisuwa, ana a Sauli.

3. Ndi nkhondoyi inamkulira Sauli, ndi amauta anampeza; ndipo anatenga nkhawa cifukwa ca amauta.

1 Mbiri 10