1 Mbiri 9:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi Azeli anali nao ana asanu ndi mmodzi, maina ao ndi awa; Azrikamu, Bokeru, ndi Ismayeli, ndi Seariya, ndi Obadiya, ndi Hanani; awa ndi ana a Azeli.

1 Mbiri 9

1 Mbiri 9:39-44