1 Mbiri 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Aisrayeli onse anasonkhana kwa Davide ku Hebroni, ndi kuti, Taonani, ife ndife pfupa lanu, ndi mnofu wanu.

1 Mbiri 11

1 Mbiri 11:1-4