1 Mbiri 11:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngakhale kale lomwe, pokhala mfumu Sauliyo, woturuka ndi kulowa nao Aisrayeli ndinu; ndipo Yehova Mulungu wanu anati kwa inu, Uzidyetsa anthu anga Aisrayeli, nukhale mtsogoleri wa anthu anga Israyeli.

1 Mbiri 11

1 Mbiri 11:1-9