1 Mafumu 20:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lace lonse la nkhondo; ndi mafumu makumi atatu mphambu awiri anali naye, pamodzi ndi akavalo ndi magareta; nakamangira Samaria misasa, naponyana nao nkhondo.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:1-3