1 Mafumu 19:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwerera panali iye uja, natengako ng'ombe ziwiri, nazipha, naphikira nyama yace ndi zipangizo za zocitira nazo ng'ombe, napatsa anthu adye. Atatero, ananyamuka, natsata Eliya, namtumikira.

1 Mafumu 19

1 Mafumu 19:11-21