1 Mafumu 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anasiya ng'ombe zija, namthamangira Eliya, nati, Ndiloleni ndithange ndakapsompsona atate wanga ndi amai wanga; nditatero ndidzakutsatani. Nati iye, Bwerera, ndakucitanji?

1 Mafumu 19

1 Mafumu 19:18-21