1 Mafumu 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika, pamene Ahiya anamva mgugu wa mapazi ace alinkulowa pakhomo, anati, Lowa mkazi iwe wa Yerobiamu, wadzizimbaitsiranji? pakuti ine ndatumidwa kwa iwe ndi mau olasa.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:4-12