1 Mafumu 14:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena ndi Ahiya, Taona, mkazi wa Yerobiamu akudza kukufunsa za mwana wace, popeza adwala; udzanena naye mwakuti mwakuti; popeza kudzakhala pakulowa iye adzadzizimbaitsa.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:2-15