1 Mafumu 14:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natero mkazi wa Yerobiamu, nanyamuka namka ku Silo, nalowa m'nyumba ya Ahiya. Koma Ahiya sanatha kupenya, popeza maso ace anali tong'o, cifukwa ca ukalamba wace.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:1-13