1 Mafumu 14:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kauze Yerobiamu, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Ndingakhale ndinakukulitsa pakati pa anthu, ndi kukukhalitsa mfumu ya anthu anga Aisrayeli,

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:4-10