Zekariya 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova: Ndabwerera kudza ku Ziyoni, ndidzakhala pakati pa Yerusalemu; ndi Yerusalemu adzachedwa, Madzi wa coonadi; ndi phiri la Yehova wa makamu, Phiri lopatulika.

Zekariya 8

Zekariya 8:1-6