Zekariya 8:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu: Ndimcitira nsanje Ziyoni ndi nsanje yaikuru, ndipo ndimcitira nsanje ndi ukali waukuru.

Zekariya 8

Zekariya 8:1-9