Zekariya 6:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akorona adzakhala wa Kelemu, ndi wa Tobiya, ndi wa Yedaya, ndi wa Keni mwana wa Zefaniya, akhale cikumbutso m'Kacisi wa Yehova.

Zekariya 6

Zekariya 6:5-15