Zekariya 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

inde adzamanga Kacisi wa Yehova; nadzasenza ulemererowo, nadzakhala ndi kulamulira pa mpando wacifumu wace; nadzakhala wansembe pampando wacifumu wace; ndi uphungu wa mtendere udzakhala pakati pa iwo awiri,

Zekariya 6

Zekariya 6:12-15