Zekariya 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ine, ati Yehova, ndidzakhala kwa iye linga lamoto pozungulira pace, ndipo ndidzakhala ulemerero m'kati mwace.

Zekariya 2

Zekariya 2:1-12