Zekariya 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena naye, Thamanga, lankhula ndi mnyamata uyu, ndi kuti, M'Yerusalemu mudzakhala anthu ngati m'midzi yopanda malinga, cifukwa ca kucuruka anthu ndi zoweta momwemo.

Zekariya 2

Zekariya 2:1-10