Zekariya 11:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinadula ndodo yanga yina, ndiyo Comanganitsa, kuti ndithetse cibale ca pakati pa Yuda ndi Israyeli.

Zekariya 11

Zekariya 11:7-17