Zekariya 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Kaziponye kwa woumba mbiya, mtengo wace wokometsetsa anandiyesawo. Ndipo ndinatenga ndarama makumi atatu asiliva, ndi kuziponya kwa woumba mbiya, m'nyumba ya Yehova.

Zekariya 11

Zekariya 11:12-17