Zekariya 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkwiyo wanga wayakira abusa, ndipo ndidzalanga atonde; pakuti Yehova wa makamu adzazonda zoweta zace, ndizo nyumba ya Yuda, nadzaziika ngati kavalo wace waulemerero kunkhondo.

Zekariya 10

Zekariya 10:1-11