Zekariya 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti aterafi anena zopanda pace, ndi aula aona bodza; nafotokoza maloto acabe, asangalatsa nazo zopanda pace; cifukwa cace ayendayenda ngati nkhosa, azunzika popeza palibe mbusa.

Zekariya 10

Zekariya 10:1-3