Zefaniya 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku ilo sudzacita manyazi ndi zocita zako zonse unandilakwira nazo; pakuti pamenepo ndidzacotsa pakati pako amene akondwera ndi kudzikuza kwako, ndipo sudzacita kudzikuzanso m'phiri langa lopatulika.

Zefaniya 3

Zefaniya 3:7-18