Zefaniya 3:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kucokera tsidya lija la mitsinje ya Kusi ondipembedza, ndiwo mwana wamkazi wa obalalika anga, adzabwera naco copereka canga.

Zefaniya 3

Zefaniya 3:9-14