Yoswa 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anaika anthu, khamu lonse lokhala kumpoto kwa mudzi, ndi olalira ao kumadzulo kwa mudzi, ndipo usiku uja Yoswa analowa pakati pa cigwa,

Yoswa 8

Yoswa 8:4-16