Yoswa 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga amuna ngati zikwi zisanu, nawaika m'molalira pakati pa Beteli ndi Ai, kumadzulo kwa mudzi.

Yoswa 8

Yoswa 8:4-20