Yoswa 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kazembe wa ankhondo a Yehova anati kwa Yoswa, Bvula nsapato yako pa phazi lako; pakuti malo upondapo mpopatulika. Nacita Yoswa comweco.

Yoswa 5

Yoswa 5:10-15