Yoswa 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, lai, koma ndadza ine, kazembe wa ankhondo a Yehova. Pamenepo Yoswa anagwa nkhope yace pansi, napembedza, nati kwa iye, Anenanji Ambuyanga kwa mtumiki wace?

Yoswa 5

Yoswa 5:11-15