Yoswa 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, Lero lino ndidzayamba kukukuza pamaso pa Aisrayeli onse, kuti adziwe, kuti monga momwe ndinakhalira ndi Mose, momwemo ndidzakhala ndi iwe.

Yoswa 3

Yoswa 3:1-11