Yoswa 3:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa ananena kwa anthu, Mudzipatule, pakuti mawa Yehova adzacita zodabwiza pakati pa inu.

Yoswa 3

Yoswa 3:1-9