Yoswa 23:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu wanu Iyeyu adzawapitikitsa pamaso panu, ndi kulanda dziko lao kuwacotsa pamaso panu, ndipo mudzalandira dziko lao likhale colowa canu; monga Yehova Mulungu wanu ananena ndi inu.

Yoswa 23

Yoswa 23:3-14